Yesaya 30:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Mzimu* wa Mulungu uli ngati mtsinje wosefukira umene wafika mʼkhosi,Kuti agwedeze mitundu ya anthu musefa wachiwonongeko.*Ndipo pakamwa pa mitundu ya anthuwo padzamangidwa zingwe ngati zowongolera hatchi,+ zimene zidzawachititse kuti asochere. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 30:28 Yesaya 1, ptsa. 313, 315
28 Mzimu* wa Mulungu uli ngati mtsinje wosefukira umene wafika mʼkhosi,Kuti agwedeze mitundu ya anthu musefa wachiwonongeko.*Ndipo pakamwa pa mitundu ya anthuwo padzamangidwa zingwe ngati zowongolera hatchi,+ zimene zidzawachititse kuti asochere.