Yesaya 30:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Koma mudzaimba nyimbo ngati imene imaimbidwa usikuMukamakonzekera* chikondwerero,+Ndipo mudzasangalala mumtima mwanu ngati munthuAmene akuyenda, kwinaku akuimba* chitoliroPopita kuphiri la Yehova, Thanthwe la Isiraeli.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 30:29 Yesaya 1, tsa. 314
29 Koma mudzaimba nyimbo ngati imene imaimbidwa usikuMukamakonzekera* chikondwerero,+Ndipo mudzasangalala mumtima mwanu ngati munthuAmene akuyenda, kwinaku akuimba* chitoliroPopita kuphiri la Yehova, Thanthwe la Isiraeli.+