-
Yesaya 30:33Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
Malo amene iye wakonzawo ndi aakulu komanso ozama
Ndipo kuli moto waukulu ndi nkhuni zambiri.
Mpweya wa Yehova, womwe uli ngati mtsinje wa sulufule,
Udzayatsa malowo.
-