Yesaya 31:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Tsoka kwa anthu amene amapita ku Iguputo kukapempha thandizo,+Amene amadalira mahatchi,+Amene amadalira magaleta ankhondo chifukwa chakuti ndi ambiri,Komanso mahatchi ankhondo* chifukwa chakuti ndi amphamvu kwambiri. Koma sayangʼana kwa Woyera wa Isiraeli,Ndipo safunafuna Yehova. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 31:1 Yesaya 1, ptsa. 317-318
31 Tsoka kwa anthu amene amapita ku Iguputo kukapempha thandizo,+Amene amadalira mahatchi,+Amene amadalira magaleta ankhondo chifukwa chakuti ndi ambiri,Komanso mahatchi ankhondo* chifukwa chakuti ndi amphamvu kwambiri. Koma sayangʼana kwa Woyera wa Isiraeli,Ndipo safunafuna Yehova.