Yesaya 32:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Munthu wamakhalidwe oipa, njira zake nʼzoipa.+Iye amalimbikitsa anthu kuchita khalidwe lochititsa manyaziNʼcholinga choti asokoneze munthu wozunzika ndi wosauka pogwiritsa ntchito mabodza,+Ngakhale pamene munthuyo akunena zoona. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 32:7 Yesaya 1, tsa. 337
7 Munthu wamakhalidwe oipa, njira zake nʼzoipa.+Iye amalimbikitsa anthu kuchita khalidwe lochititsa manyaziNʼcholinga choti asokoneze munthu wozunzika ndi wosauka pogwiritsa ntchito mabodza,+Ngakhale pamene munthuyo akunena zoona.