-
Yesaya 32:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Koma munthu wopatsa amakhala ndi zolinga zochita zinthu mowolowa manja,
Ndipo nthawi zonse zochita zake zimasonyeza kuti ndi wopatsa.
-