Yesaya 32:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Panthaka ya anthu anga padzamera zitsamba zaminga.Zidzamera panyumba zonse zimene kale zinali zodzaza ndi chisangalalo,Inde, pamzinda umene kale unali wodzaza ndi chikondwerero.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 32:13 Yesaya 1, tsa. 339
13 Panthaka ya anthu anga padzamera zitsamba zaminga.Zidzamera panyumba zonse zimene kale zinali zodzaza ndi chisangalalo,Inde, pamzinda umene kale unali wodzaza ndi chikondwerero.+