Yesaya 32:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Chifukwa nsanja yokhala ndi mpanda wolimba yasiyidwa.Mzinda waphokoso wasiyidwa.+ Ofeli+ ndi nsanja ya mlonda zasanduka chipululu mpaka kalekale.Zasanduka malo amene abulu amʼtchire akusangalalako,Komanso malo odyetserako ziweto,+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 32:14 Yesaya 1, ptsa. 339-340
14 Chifukwa nsanja yokhala ndi mpanda wolimba yasiyidwa.Mzinda waphokoso wasiyidwa.+ Ofeli+ ndi nsanja ya mlonda zasanduka chipululu mpaka kalekale.Zasanduka malo amene abulu amʼtchire akusangalalako,Komanso malo odyetserako ziweto,+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 32:14 Yesaya 1, ptsa. 339-340