Yesaya 32:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mpaka mzimu utatsanulidwa pa ife kuchokera kumwamba,+Ndiponso chipululu chitakhala munda wa zipatso,Komanso munda wa zipatsowo utayamba kuoneka ngati nkhalango.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 32:15 Yesaya 1, tsa. 340
15 Mpaka mzimu utatsanulidwa pa ife kuchokera kumwamba,+Ndiponso chipululu chitakhala munda wa zipatso,Komanso munda wa zipatsowo utayamba kuoneka ngati nkhalango.+