Yesaya 33:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Inu Yehova, tikomereni mtima.+ Chiyembekezo chathu chili pa inu. Tilimbitseni ndi dzanja lanu+ mʼmawa uliwonse.Mukhale chipulumutso chathu pa nthawi yamavuto.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 33:2 Yesaya 1, ptsa. 343-346
2 Inu Yehova, tikomereni mtima.+ Chiyembekezo chathu chili pa inu. Tilimbitseni ndi dzanja lanu+ mʼmawa uliwonse.Mukhale chipulumutso chathu pa nthawi yamavuto.+