Yesaya 33:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mʼmasiku anu, iye adzachititsa kuti muzimva kuti ndinu otetezeka.Chimene amaona kuti ndi chamtengo wapataliNdi chipulumutso chake chachikulu,+ nzeru, kudziwa zinthu komanso kuopa Yehova.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 33:6 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),1/2024, ptsa. 22-23
6 Mʼmasiku anu, iye adzachititsa kuti muzimva kuti ndinu otetezeka.Chimene amaona kuti ndi chamtengo wapataliNdi chipulumutso chake chachikulu,+ nzeru, kudziwa zinthu komanso kuopa Yehova.+