Yesaya 33:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Iye adzakhala pamalo okwera.Malo ake othawirako otetezeka* adzakhala mʼmatanthwe movuta kufikamo.Iye adzapatsidwa chakudyaNdipo madzi ake sadzatha.”+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 33:16 Yesaya 1, ptsa. 348-349
16 Iye adzakhala pamalo okwera.Malo ake othawirako otetezeka* adzakhala mʼmatanthwe movuta kufikamo.Iye adzapatsidwa chakudyaNdipo madzi ake sadzatha.”+