Yesaya 33:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Mumtima mwako udzaganizira mozama za chinthu choopsa kuti: “Kodi mlembi ali kuti? Kodi ali kuti amene ankapereka msonkho uja?+ Kodi amene ankawerenga nsanja uja ali kuti?” Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 33:18 Yesaya 1, ptsa. 349-350
18 Mumtima mwako udzaganizira mozama za chinthu choopsa kuti: “Kodi mlembi ali kuti? Kodi ali kuti amene ankapereka msonkho uja?+ Kodi amene ankawerenga nsanja uja ali kuti?”