Yesaya 33:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Anthu achipongwe simudzawaonanso,Anthu amene chilankhulo chawo nʼchovuta kumva,*Anthu achibwibwi amene simungamvetse zimene akulankhula.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 33:19 Yesaya 1, ptsa. 349-350
19 Anthu achipongwe simudzawaonanso,Anthu amene chilankhulo chawo nʼchovuta kumva,*Anthu achibwibwi amene simungamvetse zimene akulankhula.+