Yesaya 33:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Taonani Ziyoni, mzinda umene timachitiramo zikondwerero zathu.+ Maso anu adzaona kuti Yerusalemu ndi malo okhalamo abata,Tenti imene sidzachotsedwa.+ Zikhomo zake sizidzazulidwaNdipo zingwe zake sizidzadulidwa. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 33:20 Yesaya 1, ptsa. 350-351
20 Taonani Ziyoni, mzinda umene timachitiramo zikondwerero zathu.+ Maso anu adzaona kuti Yerusalemu ndi malo okhalamo abata,Tenti imene sidzachotsedwa.+ Zikhomo zake sizidzazulidwaNdipo zingwe zake sizidzadulidwa.