-
Yesaya 33:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Koma kumeneko, Yehova Wolemekezeka
Adzakhala malo a mitsinje ndi a ngalande zikuluzikulu kwa ife.
Malo amene sitima zankhondo sizidzapitako
Komanso amene sitima zikuluzikulu sizidzadutsako.
-