-
Yesaya 34:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
34 Bwerani pafupi kuti mumve, inu mitundu ya anthu,
Mvetserani, inu anthu a mitundu ina.
Dziko lapansi ndi zonse zimene zili mmenemo zimvetsere,
Nthaka yapadziko lapansi ndi zonse zimene zili pamenepo.
-