Yesaya 34:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Anthu awo ophedwa adzatayidwa,Ndipo fungo loipa la mitembo yawo lidzakwera mʼmwamba.+Mapiri adzasungunuka chifukwa cha magazi awo.*+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 34:3 Yesaya 1, ptsa. 357-358
3 Anthu awo ophedwa adzatayidwa,Ndipo fungo loipa la mitembo yawo lidzakwera mʼmwamba.+Mapiri adzasungunuka chifukwa cha magazi awo.*+