-
Yesaya 34:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Ngʼombe zamphongo zamʼtchire zidzapita nawo limodzi,
Ngʼombe zingʼonozingʼono zamphongo zidzapita limodzi ndi zamphamvu.
Dziko lawo lidzakhala magazi okhaokha,
Ndipo fumbi lamʼdziko lawo lidzanona ndi mafuta.”
-