Yesaya 34:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mitsinje yake* idzasintha nʼkukhala phula,Fumbi lake lidzakhala sulufule,Ndipo dziko lake lidzakhala ngati phula limene likuyaka. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 34:9 Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 210 Yesaya 1, tsa. 366 Chisungiko cha Padziko Lonse, tsa. 126
9 Mitsinje yake* idzasintha nʼkukhala phula,Fumbi lake lidzakhala sulufule,Ndipo dziko lake lidzakhala ngati phula limene likuyaka.