Yesaya 34:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Usiku kapena masana motowo sudzazimitsidwa.Utsi wake udzapitiriza kukwera mʼmwamba mpaka kalekale. Dzikolo lidzakhala lowonongedwa ku mibadwomibadwo.Mpaka muyaya, palibe amene adzadutsemo.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 34:10 Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 210 Yesaya 1, ptsa. 366-367 Chisungiko cha Padziko Lonse, ptsa. 126-127
10 Usiku kapena masana motowo sudzazimitsidwa.Utsi wake udzapitiriza kukwera mʼmwamba mpaka kalekale. Dzikolo lidzakhala lowonongedwa ku mibadwomibadwo.Mpaka muyaya, palibe amene adzadutsemo.+
34:10 Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 210 Yesaya 1, ptsa. 366-367 Chisungiko cha Padziko Lonse, ptsa. 126-127