-
Yesaya 34:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Mbalame ya vuwo komanso nungu zidzakhala kumeneko,
Akadzidzi a makutu ataliatali ndi akhwangwala azidzakhala kumeneko.
Mulungu adzayeza dzikolo ndi chingwe choyezera komanso miyala yoyezera
Posonyeza kuti mʼdzikoli simudzakhala aliyense komanso lidzakhala lopanda ntchito.
-