Yesaya 34:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Minga zidzamera pansanja zake zokhala ndi mpanda wolimba,Zomera zoyabwa ndi zitsamba zaminga zidzamera pamalo ake otetezeka. Iye adzakhala malo okhala mimbulu,+Ndi malo obisalamo nthiwatiwa. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 34:13 Yesaya 1, ptsa. 366-367 Chisungiko cha Padziko Lonse, ptsa. 126-128
13 Minga zidzamera pansanja zake zokhala ndi mpanda wolimba,Zomera zoyabwa ndi zitsamba zaminga zidzamera pamalo ake otetezeka. Iye adzakhala malo okhala mimbulu,+Ndi malo obisalamo nthiwatiwa.