Yesaya 34:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Nyama zamʼchipululu zidzakumana ndi nyama zolira mokuwa,Ndipo mbuzi yamʼtchire idzaitana inzake.* Inde, mbalame yotchedwa lumbe izidzakhala kumeneko ndipo idzapeza malo opumulirako. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 34:14 Yesaya 1, ptsa. 366-367 Chisungiko cha Padziko Lonse, ptsa. 126-128
14 Nyama zamʼchipululu zidzakumana ndi nyama zolira mokuwa,Ndipo mbuzi yamʼtchire idzaitana inzake.* Inde, mbalame yotchedwa lumbe izidzakhala kumeneko ndipo idzapeza malo opumulirako.