Yesaya 35:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Amene ali ndi nkhawa mumtima mwawo muwauze kuti: “Limbani mtima. Musachite mantha. Chifukwa Mulungu wanu adzabwera nʼkudzabwezera adani anu.Mulungu adzabwera kudzapereka chilango.+ Iye adzabwera ndipo adzakupulumutsani.”+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 35:4 Yesaya 1, ptsa. 372-373, 381 Nsanja ya Olonda,2/15/1996, tsa. 111/15/1988, tsa. 20
4 Amene ali ndi nkhawa mumtima mwawo muwauze kuti: “Limbani mtima. Musachite mantha. Chifukwa Mulungu wanu adzabwera nʼkudzabwezera adani anu.Mulungu adzabwera kudzapereka chilango.+ Iye adzabwera ndipo adzakupulumutsani.”+