Yesaya 36:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Mʼchaka cha 14 cha Mfumu Hezekiya, Senakeribu mfumu ya Asuri+ anabwera kudzaukira mizinda yonse ya Yuda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri, ndipo analanda mizindayo.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 36:1 Yesaya 1, ptsa. 383-385
36 Mʼchaka cha 14 cha Mfumu Hezekiya, Senakeribu mfumu ya Asuri+ anabwera kudzaukira mizinda yonse ya Yuda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri, ndipo analanda mizindayo.+