Yesaya 36:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako Eliyakimu+ mwana wa Hilikiya amene anali woyangʼanira banja lachifumu, Sebina+ mlembi ndi Yowa mwana wa Asafu wolemba zochitika, anapita kukakumana naye. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 36:3 Nsanja ya Olonda,1/15/2007, tsa. 9 Yesaya 1, ptsa. 385-386
3 Kenako Eliyakimu+ mwana wa Hilikiya amene anali woyangʼanira banja lachifumu, Sebina+ mlembi ndi Yowa mwana wa Asafu wolemba zochitika, anapita kukakumana naye.