Yesaya 36:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Choncho Rabisake anawauza kuti: “Mukauze Hezekiya kuti, ‘Mfumu yaikulu, mfumu ya Asuri yanena kuti: “Kodi ukudalira chiyani?+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 36:4 Yesaya 1, tsa. 386
4 Choncho Rabisake anawauza kuti: “Mukauze Hezekiya kuti, ‘Mfumu yaikulu, mfumu ya Asuri yanena kuti: “Kodi ukudalira chiyani?+