Yesaya 36:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ukudalira thandizo la Iguputo, bango lophwanyika loti munthu ataligwira kuti alitsamire, lingamucheke mʼmanja. Ndi mmene zilili ndi Farao mfumu ya Iguputo kwa onse omudalira.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 36:6 Yesaya 1, tsa. 386
6 Ukudalira thandizo la Iguputo, bango lophwanyika loti munthu ataligwira kuti alitsamire, lingamucheke mʼmanja. Ndi mmene zilili ndi Farao mfumu ya Iguputo kwa onse omudalira.+