Yesaya 36:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ngati mungandiuze kuti, ‘Tikudalira Yehova Mulungu wathu,’ kodi iyeyo si amene Hezekiya wamuchotsera malo ake okwezeka ndi maguwa ake ansembe+ nʼkuuza Yuda ndi Yerusalemu kuti, ‘Muzigwada patsogolo pa guwa lansembe iliʼ?”’+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 36:7 Yesaya 1, tsa. 386
7 Ngati mungandiuze kuti, ‘Tikudalira Yehova Mulungu wathu,’ kodi iyeyo si amene Hezekiya wamuchotsera malo ake okwezeka ndi maguwa ake ansembe+ nʼkuuza Yuda ndi Yerusalemu kuti, ‘Muzigwada patsogolo pa guwa lansembe iliʼ?”’+