-
Yesaya 36:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Kodi ungathe bwanji kuthamangitsa bwanamkubwa mmodzi, yemwe ndi mtumiki wotsika kwambiri wa mbuye wanga, pamene iweyo ukuchita kudalira Iguputo kuti akupatse magaleta ndi okwera pamahatchi?
-