Yesaya 36:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Atamva zimenezi, Eliyakimu, Sebina+ ndi Yowa anauza Rabisake+ kuti: “Chonde lankhulani ndi ife atumiki anu mʼchilankhulo cha Chiaramu*+ chifukwa timachimva. Musalankhule nafe mʼchilankhulo cha Ayuda, kuti anthu amene ali pamakomawa asamve.”+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 36:11 Yesaya 1, tsa. 387
11 Atamva zimenezi, Eliyakimu, Sebina+ ndi Yowa anauza Rabisake+ kuti: “Chonde lankhulani ndi ife atumiki anu mʼchilankhulo cha Chiaramu*+ chifukwa timachimva. Musalankhule nafe mʼchilankhulo cha Ayuda, kuti anthu amene ali pamakomawa asamve.”+