Yesaya 36:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Musalole kuti Hezekiya akuchititseni kudalira Yehova,+ pokuuzani kuti: “Ndithu Yehova atipulumutsa ndipo mzindawu superekedwa mʼmanja mwa mfumu ya Asuri.”
15 Musalole kuti Hezekiya akuchititseni kudalira Yehova,+ pokuuzani kuti: “Ndithu Yehova atipulumutsa ndipo mzindawu superekedwa mʼmanja mwa mfumu ya Asuri.”