Yesaya 36:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Musalole kuti Hezekiya akupusitseni ponena kuti, ‘Yehova atipulumutsa.’ Kodi pali mulungu aliyense amene wakwanitsa kupulumutsa anthu ake mʼmanja mwa mfumu ya Asuri?+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 36:18 Yesaya 1, tsa. 388
18 Musalole kuti Hezekiya akupusitseni ponena kuti, ‘Yehova atipulumutsa.’ Kodi pali mulungu aliyense amene wakwanitsa kupulumutsa anthu ake mʼmanja mwa mfumu ya Asuri?+