Yesaya 36:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Koma anthuwo anangokhala chete, osamuyankha chilichonse, chifukwa mfumu inawalamula kuti, “Musakamuyankhe.”+
21 Koma anthuwo anangokhala chete, osamuyankha chilichonse, chifukwa mfumu inawalamula kuti, “Musakamuyankhe.”+