Yesaya 36:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndiyeno Eliyakimu mwana wa Hilikiya amene ankayangʼanira banja lachifumu,* Sebina+ mlembi ndi Yowa mwana wa Asafu wolemba zochitika, anapita kwa Hezekiya atangʼamba zovala zawo ndipo anamuuza zomwe Rabisake ananena.
22 Ndiyeno Eliyakimu mwana wa Hilikiya amene ankayangʼanira banja lachifumu,* Sebina+ mlembi ndi Yowa mwana wa Asafu wolemba zochitika, anapita kwa Hezekiya atangʼamba zovala zawo ndipo anamuuza zomwe Rabisake ananena.