Yesaya 37:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Mfumu Hezekiya itangomva zimenezi, inangʼamba zovala zake nʼkuvala chiguduli. Itatero inapita mʼnyumba ya Yehova.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 37:1 Yesaya 1, ptsa. 388-390
37 Mfumu Hezekiya itangomva zimenezi, inangʼamba zovala zake nʼkuvala chiguduli. Itatero inapita mʼnyumba ya Yehova.+