Yesaya 37:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kenako inatuma Eliyakimu amene ankayangʼanira banja lachifumu,* Sebina mlembi ndi akuluakulu a ansembe, onse atavala ziguduli, kuti apite kwa mneneri Yesaya,+ mwana wa Amozi. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 37:2 Yesaya 1, ptsa. 388-390
2 Kenako inatuma Eliyakimu amene ankayangʼanira banja lachifumu,* Sebina mlembi ndi akuluakulu a ansembe, onse atavala ziguduli, kuti apite kwa mneneri Yesaya,+ mwana wa Amozi.