Yesaya 37:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iwo anamuuza kuti: “Hezekiya wanena kuti, ‘Lero ndi tsiku la zowawa,* lonyozedwa ndi lochititsidwa manyazi. Chifukwa tili ngati akazi amene atsala pangʼono kubereka,* koma alibe mphamvu zoti aberekere.+
3 Iwo anamuuza kuti: “Hezekiya wanena kuti, ‘Lero ndi tsiku la zowawa,* lonyozedwa ndi lochititsidwa manyazi. Chifukwa tili ngati akazi amene atsala pangʼono kubereka,* koma alibe mphamvu zoti aberekere.+