Yesaya 37:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno Yesaya anawauza kuti: “Mukauze mbuye wanu kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Usachite mantha+ chifukwa cha mawu amene wamva, amene atumiki a mfumu ya Asuri+ alankhula pondinyoza.
6 Ndiyeno Yesaya anawauza kuti: “Mukauze mbuye wanu kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Usachite mantha+ chifukwa cha mawu amene wamva, amene atumiki a mfumu ya Asuri+ alankhula pondinyoza.