Yesaya 37:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Rabisake atamva kuti mfumu ya Asuri yachoka ku Lakisi anabwerera kwa mfumuyo ndipo anaipeza ikumenyana ndi Libina.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 37:8 Yesaya 1, ptsa. 390-391
8 Rabisake atamva kuti mfumu ya Asuri yachoka ku Lakisi anabwerera kwa mfumuyo ndipo anaipeza ikumenyana ndi Libina.+