Yesaya 37:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “Mukauze Hezekiya mfumu ya Yuda kuti, ‘Mulungu wako amene ukumudalira asakunamize, ponena kuti: “Yerusalemu saperekedwa mʼmanja mwa mfumu ya Asuri.”+
10 “Mukauze Hezekiya mfumu ya Yuda kuti, ‘Mulungu wako amene ukumudalira asakunamize, ponena kuti: “Yerusalemu saperekedwa mʼmanja mwa mfumu ya Asuri.”+