Yesaya 37:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Hezekiya anatenga makalatawo mʼmanja mwa anthuwo nʼkuwawerenga. Kenako iye anapita nawo kunyumba ya Yehova nʼkuwatambasula pamaso pa Yehova.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 37:14 Yesaya 1, tsa. 391
14 Hezekiya anatenga makalatawo mʼmanja mwa anthuwo nʼkuwawerenga. Kenako iye anapita nawo kunyumba ya Yehova nʼkuwatambasula pamaso pa Yehova.+