Yesaya 37:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Inu Yehova wa magulu ankhondo akumwamba,+ Mulungu wa Isiraeli, wokhala pamwamba* pa akerubi, inu nokha ndinu Mulungu woona wa maufumu onse apadziko lapansi. Inuyo munapanga kumwamba ndi dziko lapansi. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 37:16 Nsanja ya Olonda,7/1/1996, tsa. 91/15/1988, ptsa. 17-18
16 “Inu Yehova wa magulu ankhondo akumwamba,+ Mulungu wa Isiraeli, wokhala pamwamba* pa akerubi, inu nokha ndinu Mulungu woona wa maufumu onse apadziko lapansi. Inuyo munapanga kumwamba ndi dziko lapansi.