Yesaya 37:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Tcherani khutu lanu, inu Yehova, mumve.+ Tsegulani maso anu, inu Yehova, muone.+ Imvani mawu onse amene Senakeribu watumiza onyoza Mulungu wamoyo.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 37:17 Nsanja ya Olonda,1/15/1988, ptsa. 17-18
17 Tcherani khutu lanu, inu Yehova, mumve.+ Tsegulani maso anu, inu Yehova, muone.+ Imvani mawu onse amene Senakeribu watumiza onyoza Mulungu wamoyo.+