Yesaya 37:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 awa ndi mawu otsutsana naye amene Yehova wanena: “Namwali, mwana wamkazi wa Ziyoni,* wakunyoza ndipo wakunyodola. Mwana wamkazi wa Yerusalemu* wakupukusira mutu. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 37:22 Yesaya 1, ptsa. 391-392
22 awa ndi mawu otsutsana naye amene Yehova wanena: “Namwali, mwana wamkazi wa Ziyoni,* wakunyoza ndipo wakunyodola. Mwana wamkazi wa Yerusalemu* wakupukusira mutu.