Yesaya 37:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Kodi sunamve? Ndinakonza kalekale zimene ndidzachite. Ndinakonza zimenezi mʼmasiku amakedzana.+ Tsopano ndizichita.+ Iweyo udzasandutsa mizinda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri kukhala milu ya mabwinja.+
26 Kodi sunamve? Ndinakonza kalekale zimene ndidzachite. Ndinakonza zimenezi mʼmasiku amakedzana.+ Tsopano ndizichita.+ Iweyo udzasandutsa mizinda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri kukhala milu ya mabwinja.+