Yesaya 37:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Anthu amʼnyumba ya Yuda amene adzapulumuke, amene adzatsale,+ adzakhala ngati mitengo imene yazika mizu pansi nʼkubereka zipatso zambiri. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 37:31 Yesaya 1, tsa. 392 Nsanja ya Olonda,8/15/1994, tsa. 31
31 Anthu amʼnyumba ya Yuda amene adzapulumuke, amene adzatsale,+ adzakhala ngati mitengo imene yazika mizu pansi nʼkubereka zipatso zambiri.