Yesaya 37:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Chifukwa anthu otsala adzachokera ku Yerusalemu ndipo opulumuka adzachokera kuphiri la Ziyoni.+ Yehova wa magulu ankhondo akumwamba adzachita zimenezi modzipereka kwambiri.+
32 Chifukwa anthu otsala adzachokera ku Yerusalemu ndipo opulumuka adzachokera kuphiri la Ziyoni.+ Yehova wa magulu ankhondo akumwamba adzachita zimenezi modzipereka kwambiri.+