Yesaya 37:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Choncho Yehova wanena izi zokhudza mfumu ya Asuri:+ “Sadzalowa mumzindawu+Kapena kuponyamo muviKapena kufikamo ndi chishangoKapenanso kumanga malo okwera omenyerapo nkhondo atauzungulira.”’+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 37:33 Yesaya 1, ptsa. 392-394
33 Choncho Yehova wanena izi zokhudza mfumu ya Asuri:+ “Sadzalowa mumzindawu+Kapena kuponyamo muviKapena kufikamo ndi chishangoKapenanso kumanga malo okwera omenyerapo nkhondo atauzungulira.”’+